Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano
Inamasulidwa kucokela ku Baibo ya Cingelezi ya NEW WORLD TRANSLATION OF THE HOLY SCRIPTURES
—Yokonzedwanso mu 2013—
“Yehova, [יהוה, YHWH] Ambuye Wamkulukulu, akunena kuti: ‘. . . Taonani! Nikulenga kumwamba kwatsopano na dziko lapansi latsopano. Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukika kapena kuvutitsa mtima wa munthu.’”
—Yesaya 65:13, 17, nwt-E; onaninso 2 Petulo 3:13.
© 2024
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
200 Watchtower Drive
Patterson, NY 12563-9205 U.S.A.
OFALITSA
WATCHTOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF NEW YORK, INC.
Wallkill, New York, U.S.A.
Baibo imeneyi, yathunthu kapena mbali yake, ikupezeka m’zinenelo zoposa 270. Kuti muone zinenelo zonse, pitani pa www.pr2711.com.
Mabaibo Onse a Cimasulilo ca Dziko Latsopano Amene Apulintidwa Alipo Pafupifupi:
250,000,000
Yocitidwa Apudeti mu August 2025
Baibo ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi.
Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano
New World Translation of the Holy Scriptures
Cinyanja (nwt-CIN)
Made in Japan
4-7-1 Nakashinden ,
Ebina City, Kanagawa-Pref,
243-0496 Japan