Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
‘Khalanibe m’Cikondi ca Mulungu’
Photo Credits:
◼ Page 134: Mixa/age fotostock
◼ Page 201: © bilderlounge/Tips RF/age fotostock
Buku ili si logulitsa. Colinga cake ndi kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene imacitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mucite copeleka, yendani pa webusaiti ya www.pr2711.com.
Baibo imene taseŵenzetsa ndi Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’buku lino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
Kupilinta kwa mu May, 2017
Cinyanja (lv-CIN)
© 2013, 2014
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania