LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 14 masa. 30-31
  • Kodi Mungaonetse Bwanji Kuti Ndinu Okhulupilika kwa Yehova?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mungaonetse Bwanji Kuti Ndinu Okhulupilika kwa Yehova?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 14
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kodi N’dzipeleke Kwa Mulungu Kuti N’kabatizike?
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Cikondi Ca Mulungu N’camuyaya
    Mmene Tingakhalilebe mu Cikondi ca Mulungu
  • Kukonda Yehova na Kum’yamikila Kudzakusonkhezelani Kubatizika
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Onaninso Zina
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 14 masa. 30-31

GAO 14

Kodi Mungaonetse Bwanji Kuti Ndinu Okhulupilika kwa Yehova?

Khalani kumbali ya Mulungu. 1 Petulo 5:6-9

Mkhristu akana kutengako mbali m’miyambo ya cipembedzo ndi ya ndale

Muzipewa miyambo yonse imene simagwilizana ndi Baibo. Kuti mucite zimenezi, muyenela kulimba mtima.

Musaziloŵa m’ndale; sizimacilikiza Yehova ndi Ufumu wake.

  • Yehova amachinjiliza anthu okhulupilika kwa iye.—Salimo 97:10.

Sankhani mwanzelu—mvetselani kwa Mulungu. Mateyu 7:24, 25

Munthu wapita kukasonkhana ku Nyumba ya Ufumu, kenako aphunzila Baibo na wa Mboni za Yehova

Gwilizanani ndi Mboni za Yehova; zidzakuthandizani kuyandikila kwa Mulungu.

Pitilizani kuphunzila za Mulungu ndi kuyesa-yesa kumvela malamulo ake.

Munthu akudzipeleka kwa Yehova m’pemphelo ndipo pambuyo pake akubatizika

Cikhulupililo canu cikalimba, muyenela kudzipeleka kwa Yehova ndi kubatizika.—Mateyu 28:19.

Mvetselani kwa Mulungu. Ŵelengani Baibo, ndi kufunsa Mboni za Yehova kuti zikuthandizeni kuimvetsetsa. Ndipo seŵenzetsani zimene mukuphunzila. Mukacita zimenezi, mudzakhala ndi moyo wamuyaya.—Salimo 37:29.

  • Lapani kuti mukhululukidwe.—Machitidwe 3:19.

  • Yendani panjila ya kumoyo.—Mateyu 7:13, 14.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani