Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Zimene Ndimaphunzila m’Baibo
© 2013
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA. All Rights Reserved
Ofalitsa
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA NPC. 1 Robert Broom Drive East, Rangeview,Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Kusindikiza kwa mu February 2013
Kabuku aka si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’kabuku kano tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
[Cithunzi papeji 2]
1
[Cithunzi papeji 2]
2
[Cithunzi papeji 2]
3
[Cithunzi papeji 2]
4
[Cithunzi papeji 2]
5
[Cithunzi papeji 2]
6