Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Ufumu wa Mulungu Ukulamulila
Buku ili si yogulitsa. Colinga cake ndi kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mucite copeleka, yendani pa webusaiti ya www.pr2711.com
Baibulo limene taseŵenzetsa ndi Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa lina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’buku lino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
Photo Credits: Peji 178: 1879 Songs of the Bride: Courtesy of the Pitts Theology Library, Candler School of Theology, Emory University
Kupulinta kwa mu January 2016
Cinyanja (kr-CIN)
© 2014
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA