Tsamba la Mutu wa Buku/Tsamba la Ofalitsa
Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo A baibo Okambilana Komanso Zocita
“Olungama adzalandila dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.”—Salimo 37:29.
Photo Credits: Page 15: Image © Homo Cosmicos/ Shutterstock; page 17: NASA, ESA and the Hubble Heritage Team (STScI/AURA)-ESA/Hubble Collaboration. Licensed under CC BY 4.0 (http://creativecommons.org/ licenses/by/4.0/). Source: https://esahubble.org/images/ heic0702a/; page 56: Photo by US Signal Corps/The LIFE Picture Collection via Getty Images; page 76: Château de Versailles, France/Bridgeman Images; pages 103 and 131: Based on NASA/Visible Earth imagery; page 163: © SINGLECELL ANIMATION LLC/Science Source; page 183: Daniel Osterkamp/Moment/Getty Images
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.
Mabuku onse ochulidwa muno ni olembedwa na Mboni za Yehova.
Buku lino si logulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa mwa zopeleka zaufulu. Kuti mutumize copeleka canu, pitani pa donate.jw.org.
Cinyanja (lff-CIN)
Inapulintidwa mu July 2023
© 2021 WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA