Zamkati
September 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. All rights reserved.
NKHANI ZOPHUNZILA
OCTOBER 28, 2013–NOVEMBER 3, 2013 | TSAMBA 7 • NYIMBO: 64, 114
Zikumbutso za Yehova Ndi Zodalilika
NOVEMBER 4-10, 2013 | TSAMBA 12 • NYIMBO: 116, 52
Kondwelani Ndi Zikumbutso za Yehova
Yehova nthawi zonse amagwilitsila nchito zikumbutso kuti atsogolele anthu ake. Kodi zikumbutso zimenezi zimaphatikizapo ciani? Nkhani yoyamba ifotokoza zifukwa zimene zingatipangitse kudalila zikumbutso za Mulungu. Yaciŵili idzafotokoza njila zitatu za mmene tingakhalile ndi cidalilo colimba pa zikumbutso za Yehova.
NOVEMBER 11-17, 2013 | TSAMBA 17 • NYIMBO: 69, 106
NOVEMBER 18-24, 2013 | TSAMBA 22 • NYIMBO: 27, 83
Pangani Zosankha Zanu Mwanzelu
Mmene tinaleledwela ndiponso anthu amene timakhala nao zimatikhudza maganizo athu ndi zosankha zathu. Kodi tingacite ciani kuti zosankha zathu zikhale zogwilizana ndi cifunilo ca Mulungu? Nanga n’ciani cingatithandize kucita zinthu mogwilizana ndi zosankha zathu? Nkhani zimenezi zidzatithandiza kudzipenda moona mtima pa mbali zimenezi.
NOVEMBER 25, 2013–DECEMBER 1, 2013 | TSAMBA 27 • NYIMBO: 95, 104
Upainiya Umalimbitsa Unansi Wathu ndi Mulungu
M’nkhani iyi tidzakambilana njila 8 zoonetsa mmene upainiya umalimbitsila ubwenzi wa Mkristu ndi Yehova. Ngati ndinu mpainiya, n’ciani cingakuthandizeni kuti mupitilize ngakhale mukumane ndi mavuto? Ngati mufuna kuyamba upainiya ndi kusangalala ndi madalitso ake, kodi mungacite ciani?
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
N’cifukwa Ciani Anthu Akuvutika Kwambili? 3