LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp17 na. 6 tsa. 16
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Aramagedo n’ciani?
  • Kodi n’zotheka kupulumuka nkhondo ya Aramagedo?
  • Kodi Nkhondo ya Aramagedo N’ciyani?
    Kuyankha Mafunso Okhudza Baibo
  • Aramagedo ni Nkhani Yokondweletsa!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kodi Aramagedo Idzayambila ku Israel?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?
    Nkhani Zina
  • Andale Akucenjeza za Aramagedo—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?
    Nkhani Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
wp17 na. 6 tsa. 16
“Khamu lalikulu” la anthu ocokela m’mitundu yonse apulumuka Aramagedo

“Khamu lalikulu” la anthu osaŵelengeka, ocokela m’mitundu yonse adzapulumuka pa Aramagedo

Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Kodi Aramagedo n’ciani?

Anthu ena amakhulupilila kuti . . .

idzakhala nkhondo ya zida za nyukiliya, kapena kusintha kwa nyengo kowononga cilengedwe. Imwe muganiza bwanji?

Zimene Baibo imakamba

Aramagedo ni malo ophiphilitsa oimila “nkhondo ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse.” Nkhondo yowononga anthu oipa.—Chivumbulutso 16:14, 16.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Mulungu adzamenya nkhondo ya Aramagedo osati kuti awononge dziko, koma kuti aliteteze kwa anthu amene akuliwononga.—Chivumbulutso 11:18.

  • Nkhondo ya Aramagedo idzathetsa nkhondo zonse.—Salimo 46:8, 9.

Kodi n’zotheka kupulumuka nkhondo ya Aramagedo?

Kodi mungayankhe bwanji?

  • Inde

  • Iyai

  • Kapena

Zimene Baibo imakamba

“Khamu lalikulu” la anthu ocokela m’mitundu yonse lidzapulumuka “cisautso cacikulu,” cimene cidzathetsedwa pa nkhondo ya Aramagedo.—Chivumbulutso 7:9, 14.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Mulungu afuna kuti anthu ambili akapulumuke Aramagedo. Iye amawononga anthu oipa ngati palibe mwina mocitila.—Ezekieli 18:32.

  • Baibo ifotokoza zimene tingacite kuti tikapulumuke Aramagedo.—Zefaniya 2:3.

Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani 8 m’buku iyi, Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, yofalitsidwa na Mboni za Yehova

Buku imeneyi ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani