Magazini Yophunzila
MAY 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: JULY 3-30, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
ECUADOR
Mpainiya wanthawi zonse alalikila mzimayi wamalonda m’citundu ca Cikwichuwa (Imbabura), pa msika wogulitsila nsalu mumzinda wa Otavalo, kumpoto kwa dziko la Ecuador.
OFALITSA
90,110
MAPHUNZILO A BAIBO
148,637
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
274,593
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.