Ndandanda ya Mlungu wa July 29
MLUNGU WA JULY 29
Nyimbo 51 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 26 ndime 16-22 ndi bokosi patsamba 209 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Macitidwe 26-28 (Mph. 10)
Na. 1: Macitidwe 26:19-32 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Akristu Okhulupilika Adzatengedwa Kupita Kumwamba Mobisa Asanafe?—rs tsa. 215 ndime 2 mpaka tsa. 216 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Tingadziŵe Bwanji Kuti Mzimu Woyela wa Mulungu Ukugwila Nchito Mwa Atumiki Ake?—Agal. 5:22, 23; Chiv. 22:17 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 96
Mph. 10: Lalikilani Mwacibadwa. NKhani yocokela m’buku la Sukulu ya Utumiki, patsamba 128, ndime 1, mpaka tsamba 129, ndime 1. Mwacidule funsani wofalitsa waluso amene athetsa manyazi. Kodi n’ciani camuthandiza kuti asazicita manyazi muulaliki?
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambilana, yokambidwa ndi mkulu.
Mph. 10: Musonyeze Kuti Ndinudi Ana a Atate Wanu Wakumwamba. (Mat. 5:43-45) Nkhani yokambilana yocokela mu Nsanja ya Olonda June 15, 2010, tsamba 25, ndime 1-2 ndi tsamba 27 mpaka 29, ndime 11 mpaka 18. Pemphani omvela kuti anene maphunzilo amene aphunzilapo.
Nyimbo 80 ndi Pemphelo