LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 9/13 tsa. 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa September 16
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumitu
  • MLUNGU WA SEPTEMBER 16
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 9/13 tsa. 2

Ndandanda ya Mlungu wa September 16

MLUNGU WA SEPTEMBER 16

Nyimbo 21 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:

jl tsa. 3 ndi phunzilo 1 mpaka 2 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibo: 2 Akorinto 1-7 (Mph. 10)

Na. 1: 2 Akorinto 1:15 mpaka 2:11 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: Kodi Pali Kusiyana Kotani Pakati pa Cikhulupililo Cakuti Munthu Akafa Amakabadwanso Kwinakwake, Ndi Ciyembekezo ca M’Baibo?—rs tsa. 177 ndime 4-tsa. 178 ndime 1 (Mph. 5)

No. 3: Kodi Munthu Angatani Kuti Apeze Citetezo M’dzina la Yehova?—Zef. 3:12 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 41

Mph. 10: Acinyamata—Kodi Moyo Wanu Mudzaugwilitsila Nchito Bwanji?—Gawo 2. Nkhani yocokela m’kapepala kauthenga kakuti, Moyo Wanu, ndime 10 mpaka kumapeto. Mwacidule funsani munthu amene anacita utumiki wanthawi zonse ali wacinyamata. Kodi n’ciani cinam’thandiza kuti asankhe utumiki? Kodi wapeza madalitso otani?

Mph. 10: Ngati Muli Nokha Polalikila. Kukambitsilana. (1) Ngati tilibe mnzathu wolalikila naye, n’ciani cingatithandize kukhalabe osangalala? (2) Kodi ndi macenjezo ati amene tiyenela kukumbukila tikamapanga maulendo obwelelako tili tokha? (3) Ngati palibe kagulu kamene kamakumana pamasiku amene timapita mu ulaliki, kodi tingalimbikitse bwanji ena mumpingo kuti azipita nafe? (4) Kodi pali ubwino wotani ngati nthaŵi zina tisankha kulalikila tili tokha panthawi yabwino ndiponso kumene kulibe ciopsezo ciliconse?

Mph. 10: “Ndani Amene Akucita Cifunilo ca Yehova Masiku Ano?” Mafunso ndi Mayankho. Mwacidule kambitsilanani mmene kabukuka kalili.—Onani Utumiki Wathu wa Ufumu wa March 2013, tsamba 3.

Nyimbo 107 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani