Ndandanda ya Mlungu wa November 18
MLUNGU WA NOVEMBER 18
Nyimbo 20 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
jl Phunzilo 26 mpaka 28 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Aheberi 9 mpaka 13 (Mph. 10)
Na. 1: Aheberi 10:19-39 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Kukhala Paubwenzi Ndi Mulungu N’Kofunikadi?—rs tsa. 88 ndime 4-5 (Mph. 5)
Na. 3: Njila Zimene Tingalimbikitsile Ena—Aroma 15:4; 2 Akor. 1:3, 4 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 10
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Kukambilana. Pambuyo pake, dziŵitsani mpingo za mmene nchito yapadela yogaŵila kapepala ka Uthenga wa Ufumu Na. 38 ikuyendela.
Mph. 10: “Ndabwela pano kuti . . .” Kukambilana. Pambuyo pake, chulani cogaŵila ca mwezi wa December ndipo citani citsanzo cimodzi kapena ziŵili mogwilitsila nchito nkhani yocokela m’cofalitsa cimeneco.
Mph. 10: Yehova Amamva Mapemphelo a Atumiki Ake. (1 Yoh. 3:22) Kukambilana kocokela mu buku lapacaka la 2013 tsamba 91 ndime 3, mpaka 92 ndime 1, ndi tsamba 108 mpaka 109. Pemphani omvela kuti afotokoze zimene aphunzilapo.
Nyimbo 56 ndi Pemphelo