Zilengezo
◼ Zogaŵila za mu: December: Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, kapena kapepala kakuti Kodi Mufuna Kudziŵa Mayankho Azoona pa Mafunso Aya? January ndi February: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu! kapena kamodzi ka tumabuku twa masamba 32 totsatilatu: Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kapena kakuti Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu, Mvetselani kwa Mulungu ndi kakuti Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. March: Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani!
◼ Cikumbutso ca mu 2015 cidzacitika pa Cisanu, April 3, 2015.
◼ Zofalitsa Zatsopano: Mungayambe kuoda kabuku kakuti Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya ndi kapepala kauthenga kakuti Mayankho Azoona—Pa DVD m’Cinenelo Camanja ca mu Zambia.