LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 12/13 tsa. 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa January 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa January 6
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumitu
  • MLUNGU WA JANUARY 6, 2014
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 12/13 tsa. 4

Ndandanda ya Mlungu wa January 6

MLUNGU WA JANUARY 6, 2014

Nyimbo 132 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:

jr mutu 2 ndime 20-27, ndi bokosi patsamba 29 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibo: Genesis 1–5 (Mph. 10)

Na. 1: Genesis 4:1-16 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: Anthu Amene Ali m’Cipembedzo Coona Amalalikila za Ufumu wa Mulungu Mwakhama—rs tsa. 90 ndime 4 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Mkristu Ayenela Kucita Ciani Akasemphana Maganizo ndi Mkristu Mnzake pa Nkhani za Bizinesi?—lv tsa. 222-223 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 125

Mph. 10: Zimene Mungakambe Pogaŵila Magazini mu January. Kukambilana. Fotokozani cifukwa cake magazini awa adzakhala okopa anthu a m’gawo lanu. Citani zimenezi kwa tumphindi 30 mpaka 60. Ndiyeno, pa nkhani zoyambilila zogwilizana ndi mutu wa pacikuto ca Nsanja ya Mlonda, pemphani omvela kuti achule funso lodzutsa cidwi limene angafunse poyambitsa makambilano, ndi lemba limene angaŵelenge. Citani cimodzi-modzi ndi Galamukani! ndipo ngati nthawi ilola, citaninso cimodzi-modzi ndi nkhani ina imodzi ya mu Nsanja ya Mlonda kapena Galamukani! Citani zitsanzo ziŵili za mmene mungagaŵilile magazini iliyonse.

Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.

Mph. 10: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Ŵelengani 1 Akorinto 9:19-23, ndipo kambilanani mmene lembali lingatithandizile mu ulaliki.

Nyimbo 7 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani