Zilengezo
◼ Cogaŵila ca April: Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! May, ndi June: Zimene Baibo Limaphunzitsa M’ceni-ceni, kapena kamodzi mwa tumapepala twauthenga utu: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji? Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo? Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele? Kodi Ndani Maka-Maka Amene Akulamulila Dzikoli? ndi Kodi Mavuto Adzathadi?, ndi kakuti Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo? July: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu.