Ndandanda ya Mlungu wa June 23
MLUNGU WA JUNE 23
Nyimbo 109 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 10 ndime 8 mpaka 13 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Levitiko 10-13 (Mph. 10)
Na. 1: Levitiko 12:1–13:8 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Zoona Zake za Kulambila Zinthu za Kale ndi Zifanizo za “Oyela Mtima”—rs tsa. 333 ndime 1–tsa 334 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Yehova—Amadana ndi Mau Otukwana—Iv tsa. 136-137 ndime 9-12 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 82
Mph. 10: Zogaŵila mu July. Kukambilana. Mwacidule kambilanani nkhani zimene zili mu zofalitsa zimene tidzagaŵila. Ndiyeno citani citsanzo cimodzi kapena ziŵili.
Mph. 20: “Mmene Tingathandizile Anthu Amene Amavutika Kuŵelenga.” Mafunso ndi Mayankho.
Nyimbo 55 ndi Pemphelo