Ndandanda ya Mlungu wa August 18
MLUNGU WA AUGUST 18
Nyimbo 78 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 12 ndime 14 mpaka 19, bokosi pa tsa. 148 (Mph. 30)
Msonkhano wa Nchito:
Kuŵelenga Baibulo: Numeri 10-13 (Mph. 10)
Na. 1: Numeri 10:1-16 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Cifukwa Cake Cikhulupililo Ciyenela Kukhala ndi Nchito—rs tsa. 97 ndime 1-4 (Mph. 5)
Na. 3: Dina ndi Citsanzo Coticenjeza—lv tsa. 102-103 ndime 13-15 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 74
Mph. 15: “Zaka 100 Zolengeza Ufumu”—Mbali 1. (Ndime 1-3) Nkhani yokambilana yocokela pa ndime zitatu zoyambilila ndiponso mu Nsanja ya Mlonda ya January 1, 2014 masamba 13-15 ndime 7-11. Mukafunsa funso la m’ndime 3, funsani ofalitsa aŵili amene akhala Mboni kwa nthaŵi yaitali. Apempheni kuti afotokoze zocitika za mu ulaliki nthawi yoyamba imene anakhala ofalitsa.
Mph. 15: “Zaka 100 Zolengeza Ufumu”—Mbali 2. (Ndime 4-6) Mafunso ndi mayankho. Pokambilana ndime 5 ndi 6, funsani apainiya aŵili kuti afotokoze zimene zawathandiza kukwanitsa kucita utumiki wa nthawi zonse.
Nyimbo 103 ndi Pemphelo