Zilengezo
◼ Cogaŵila ca mu August: Nchito yapadela yogaŵila kapepala kauthenga katsopano kotsatsa Webu saiti ya jw.org. September ndi October: Magazini ya Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! November: Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni kapena kamodzi ka tumapepala twauthenga utu: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?, Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?, Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?, Kodi Ndani Maka-Maka Amene Akulamulila Dzikoli?, Kodi Mavuto Adzathadi?, ndi kakuti Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?