LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 8/14 tsa. 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 1

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa September 1
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Tumitu
  • MLUNGU WA SEPTEMBER 1
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 8/14 tsa. 4

Ndandanda ya Mlungu wa September 1

MLUNGU WA SEPTEMBER 1

Nyimbo 46 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 13 ndime 1 mpaka 7 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Numeri 17-21 (Mph. 10)

Na. 1: Numeri 17:1-13 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: Mmene Timadziŵila kuti Kulidi Mdyelekezi—rs tsa. 352 ndime 1–tsa. 353 ndime 1 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Ndani Amene Ali M’manda Acikumbutso—bh tsa. 72-73 ndime 16-20 (Mph. 5)

Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 98

Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu September. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo amene ali pa tsamba lino. Ndiyeno kambilanani mmene citsanzo ciliconse cinalili.

Mph. 10: Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani omvela kuti anene mmene anapindulila ndi nkhani yakuti “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulankhula za Ufumu Molimba Mtima.” Kenako pemphani omvela kuti afotokoze mmene kunalili kovuta kwa io kulankhula za Ufumu molimba mtima. N’ciani cimene cinawathandiza kuti akwanitse kulankhula molimba mtima?

Mph. 10: Lipoti la Kampeni Yathu Yapadela. Nkhani yokambidwa ndi woyang’anila nchito. Fotokozani mwacidule mfundo zimene zili mu Utumiki Wathu wa Ufumu uno zokhudza kufunika kopitiliza kulengeza za Ufumu. Kodi mpingo unacita motani pa nkhani imeneyi? Ndi zinthu zapadela ziti zimene zinacitika pogwila nchito imeneyi?

Nyimbo 45 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani