LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 10/14 tsa. 3
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 27

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 27
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Tumitu
  • MLUNGU WA OCTOBER 27
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 10/14 tsa. 3

Ndandanda ya Mlungu wa October 27

MLUNGU WA OCTOBER 27

Nyimbo 5 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 15 ndime 7 mpaka 12 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Deuteronomo 11-13 (Mph. 10)

Kubweleza za m’Sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)

Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 45

Mph. 15: “Mmene Tingakhalile Acangu pa Nchito Yolalikila.” Nkhani yokambilana. Citani citsanzo coonetsa wofalitsa akugaŵila buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa kapena kapepala ka uthenga.

Mph. 15: Konzekelani Bwino Kuti Mulalikile Mwacangu. Nkhani yokambilana yocokela mu Nsanja ya Mlonda ya August 15, 2014 masamba 14 ndi 15, ndime 14-20. Pemphani omvela kuti achule nkhani zimene zimadetsa nkhawa anthu m’gawo lao. Kodi tingakambilane bwanji ndi anthu nkhani zimenezo? Pemphani apainiya aŵili kapena anthu okwatilana kuti acite citsanzo ca mmene angakonzekelele ulaliki wogwila mtima m’gawo lao. Acitsanzo angasankhe cofalitsa cimene adzagwilitsila nchito.

Nyimbo 95 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani