Ndandanda ya Mlungu wa December 1
MLUNGU WA DECEMBER 1
Nyimbo 34 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 1 ndime 18 mpaka 23 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Deuteronomo 32-34 (Mph. 10)
Na. 1: Deuteronomo 32:22-35 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Munthu Akafa Mzimu Wake Kapena Kuti Moyo Wake Supitilizanso Kukhala Ndi Moyo—rs tsa. 297 ndime 1–tsa. 299 ndime 3 (Mph. 5)
Na. 3: Kucita Cigololo Ndi Kucimwila Mulungu—lv tsa. 128-129 ndime 16-19 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 128
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu December. Kukambilana. Citani zitsanzo zitatu pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo amene ali pa tsamba lino. Pambuyo pa citsanzo ciliconse, pemphani omvela kuti akambe cifukwa cake nkhaniyo idzakhala yogwila mtima m’gawo lanu.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Mph. 10: Kodi Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani ofalitsa kuti akambe mmene anapindulila pogwilitsila nchito mfundo za m’nkhani yakuti “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuonetsa Anthu Cidwi.” Pemphani omvela kuti asimbe zocitika zabwino za mu ulaliki.
Nyimbo 119 ndi Pemphelo