Ndandanda ya Mlungu wa April 13
MLUNGU WA APRIL 13
Nyimbo 134 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 8 ndime 1-8 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Samueli 19-22 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 21:10–22:4 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Baranaba—Mutu: Khalani Okoma Mtima—w14 6/1 tsa. 24 ndime 13 (Mph. 5)
Na. 3: N’cifukwa Ciani Anthu Amavutika?—igw-CIN tsa 15 ndime 1-4 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: Yendani monga anthu anzelu mwa ‘kugwilitsila nchito bwino nthawi yanu.’—Aef. 5:15, 16.
Nyimbo 115
Mph. 10: Yendani Monga Anthu Anzelu mwa “Kugwilitsila Nchito Bwino Nthawi yanu.” Nkhani yofotokoza lemba la mwezi.—Aef. 5:15, 16; onani Nsanja ya Olonda ya, May 15, 2012, mas. 19-20, ndime 11-14.
Mph. 20: “Muzigwilitsa Nchito Bwino Nthawi Yanu mu Ulaliki.” Kukambilana.
Nyimbo 98 ndi Pemphelo