Zilengezo
◼ April: Gaŵilani Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! May ndi June: Gaŵilani buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, kapena kamodzi ka tumapepala twa uthenga utu: Kodi Baibo mumaiona bwanji?, Kodi zinthu zidzakhala bwanji mtsogolo? Kodi cofunika n’ciani kuti banja likhale la mtendele?, Kodi ndani maka-maka amene akulamulila dzikoli?, Kodi mavuto adzathadi? ndi kakuti Kodi n’zoona kuti akufa angakhalenso ndi moyo? July: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu
Zofalitsa Zatsopano Zimene Zilipo:
Mfundo za m’Mau a Mulungu—Mambwe-Lungu
Zimene Ndimaphunzila m’Baibo—Mambwe-Lungu
◼ Kuyambila ndi magazini ya July 1, 2015, Nsanja ya Mlonda izipezeka m’Cilamba.