Ndandanda ya Mlungu wa August 17
MLUNGU WA AUGUST 17
Nyimbo 5 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 14 ndime 1-9 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 1-4 (Mph. 8)
Na. 1: 2 Mafumu 1:11-18 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Dina—Mutu: Kugwilizana ndi Anthu Oipa Kumabweletsa Mavuto—w10 6/15 tsa. 8-9 ndime 13-15 (Mph. 5)
Na. 3: Zimene Tiyenela Kucita Kuti Tiyandikile Mulungu—igw-CIN tsa. 28 ndime 5–tsa. 29 ndime 1-3 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikila Yehova.”—Yoswa 24:15.
Nyimbo 52
Mph. 15: “Makolo—Wetani Ana Anu.” Nkhani yokambilana yocokela mu Nsanja ya Mlonda ya September 15, 2014 masamba 17 mpaka 21. Kambani mau oyamba acidule, kenako kambilanani mfundo zikuluzikulu za m’nkhaniyi zimene makolo angagwilitsile nchito.
Mph 15: Kodi Anagwila Bwanji Dzanja Lanu? (Yes 41:13)Funsani mafunso wofalitsa mmodzi kapena aŵili amene atumikila mokhulupilika kwa zaka zambili, kuti afotokoze mmene Yehova wawathandizila kulimbana ndi mavuto pomutumikila.
Nyimbo 88 ndi Pemphelo