Ndandanda ya Mlungu wa September 28
MLUNGU WA SEPTEMBER 28
Nyimbo 73 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 16 ndime 1-9 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 23-25 (Mph. 8)
Na. 1: 2 Mafumu 23:8-15 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Angelo Amagwila Nchito Yanji Pokwanilitsa Cifunilo ca Mulungu? (Mph. 5)
Na. 3: Muzitumikila Yehova Mokhulupilika—(w11 7/15 tsa. 31 ndime 16) (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Kucitila umboni mokwanila za uthenga wabwino.”—Machitidwe 20:24.
Nyimbo 93
Mph. 10: Paulo ndi Atumiki Anzake Anacitila Umboni Mokwanila ku Filipi. Kukambilana. Ŵelengani Machitidwe 16:11-15. Kambilanani mmene lembali lingatithandizile mu ulaliki.
Mph. 20: “Kugwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Pophunzitsa.” Mafunso ndi mayankho. Pambuyo pokambilana ndime 3, citani citsanzo cokonzedwa bwino coonetsa wofalitsa akugaŵila kabuku ka Uthenga Wabwino ndipo akukambilana ndime imodzi.
Nyimbo 114 ndi Pemphelo