Ndandanda ya Mlungu wa November 23
MLUNGU WA NOVEMBER 23
Nyimbo 26 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
ia mutu 3 ndime 1-13, ndi bokosi pa tsa. 29 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Mbiri 1-5 (Mph. 8)
Na. 1: 2 Mbiri 3:14–4:6 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Inoki—Mutu: Muziyenda Ndi Mulungu—w11 11/15 tsa.16 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Pali Mitundu Ingati ya Ubatizo? (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Ineyo ndinabzala, Apolo anathilila, koma Mulungu ndiye anakulitsa.”—1 Akor. 3:6.
Nyimbo 47
Mph.10: “Kukonzekela n’Kofunika Kuti Tiziphunzitsa Mwaluso.” Nkhani.
Mph.10: Kukhala ndi Khalidwe Labwino Kumatithandiza Kubzala Mbeu za Coonadi. Kukambilana kocokela m’Buku Lapacaka la 2015 tsamba 49 ndime 3 mpaka tsamba 51 ndime 3, ndi tsamba 140 ndime 3 mpaka tsamba 141 ndime 3. Pemphani omvela kuti akambe zimene aphunzilapo.
Mph.10: “Seŵenzetsani Zinthu Zopezeka m’Buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa Mogwila Mtima.” Kukambilana. Mucitenso citsanzo cacidule.
Nyimbo 123 ndi Pemphelo