LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsa. 2
  • August 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 August tsa. 2

August 1-7

MASALIMO 87–91

  • Nyimbo 49 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe m’Malo Otetezeka a Wam’mwambamwamba”: (Mph. 10)

    • Sal. 91:1, 2—‘Malo Acitetezo’ a Yehova amatithandiza kukhala otetezeka mwauzimu (w10 2/15-CN, tsa. 26-27 ndime 10-11)

    • Sal. 91:3—Mofanana ndi wosaka mbalame, Satana amafuna kutikola (w07 10/1-CN, tsa. 26-30 ndime 1-18)

    • Sal. 91:9-14—Yehova ndi malo athu acitetezo (w10 1/15-CN, tsa. 10-11 ndime 13-14; w01 11/15-CN, tsa. 19-20 ndime 13-19)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 89:34-37—Kodi mavesi amenewa akamba za pangano liti? Nanga Yehova anapeleka fanizo labwanji pofuna kuonetsa kuti panganolo n’lodalilika? (w14 10/15 tsa.10 ndime 14; w07 7/15-CN, tsa. 32 ndime 3-4)

    • Sal. 90:10, 12—Kodi tingaŵelengele bwanji “masiku athu kuti tikhale ndi mtima wanzelu”? (w06 7/15-CN, tsa. 13 ndime 4; w01 11/15-CN, tsa. 13 ndime 19)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 90:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani mavidiyo a maulaliki acitsanzo, ndipo kambilanani mfundo zake. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wawo.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 141

  • Zosoŵa za pampingo: (Mph. 5)

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuthandiza Ophunzila Baibulo Kuti Adzipeleke ndi Kubatizika”: (Mph. 10.) Kukambilana. Funsani wofalitsa amene anathandizapo munthu wina kupita patsogolo mpaka kudzipeleka ndi kubatizika. Seŵenzetsani mafunso otsatilawa: Kodi wophunzila wanu munamuthandiza bwanji kuti ayambe kukonda kwambili Yehova? Nanga munamuthandiza bwanji kukwanilitsa zolinga zake zauzimu?

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 21 ndime 1-12

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 137 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani