LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 3
  • April 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Tumitu
  • UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 3

April 9-15

MATEYU 27-28

  • Nyimbo 69 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Pitani Mukapange Ophunzila—Cifukwa ciani, Kuti, ndipo Motani?”: (10 min.)

    • Mat. 28:18—Yesu ali na ulamulilo waukulu (w04 7/1 peji 8 pala. 4)

    • Mat. 28:19—Yesu analamula kuti tilalikile na kuphunzitsa anthu pa dziko lonse (“mukaphunzitse anthu” “anthu a mitundu yonse” nwtsty mfundo zounikila)

    • Mat. 28:20—Tifunika kuthandiza anthu kudziŵa na kuseŵenzetsa zonse zimene Yesu anatiphunzitsa (“kuwaphunzitsa” nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 27:51—Kodi kung’ambika pakati kwa nsalu yochinga kunatanthauza ciani? (“nsalu yochinga,” “nyumba yopatulika” nwtsty mfundo zounikila)

    • Mat. 28:7—Kodi mngelo wa Yehova anawalemekeza bwanji azimayi amene anapita ku manda a Yesu? (“mukauze ophunzila ake kuti wauka kwa akufa” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 27:38-54

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) g17.2 peji 14—Mutu: Kodi Yesu anafera pamtanda?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 70

  • “Kulalikila na Kuphunzitsa—N’kofunika pa Nchito Yopanga Ophunzila”: (15 min.) Kukambilana. Pokambilana nkhaniyi, tambitsani vidiyo yakuti Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”—Ulaliki Wamwayi, Kunyumba ndi Nyumba, ndi yakuti Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”—Ulaliki Wapoyela, Kupanga Ophunzila.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 16

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 73 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani