LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsa. 6
  • August 27–September 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 27–September 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 August tsa. 6

August 27–September 2

LUKA 23-24

  • Nyimbo 130 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Muzikhala Okonzeka Kukhululukila Ena”: (10 min.)

    • Luka 23:34—Yesu anakhululukila asilikali aciroma amene anamukhomelela pa mtengo (cl peji 297 pala. 16)

    • Luka 23:43—Yesu anakhululukila munthu wocita zoipa (g 2/08 peji 11 mapa. 5-6)

    • Luka 24:34—Yesu anakhululukila Petulo (cl mape. 297-298 mapa. 17-18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 23:31—Kodi Yesu ayenela kuti anali kukamba za ndani pa vesiyi? (“pamene mtengo uli wauŵisi, . . . mtengowo ukadzauma” nwtsty mfundo younikila)

    • Luka 23:33—Kodi zinthu zakale zofukulidwa zionetsa bwanji kuti misomali anali kuiseŵenzetsa popha munthu mwa kum’khomelela pamtengo? (“Msomali mu fupa la kadendene” nwtsty zithunzi)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 23:1-16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo ca mu Thuboksi yathu, mogwilizana na zosoŵa za mwininyumba.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 4 mapa. 3-4

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 20

  • “Yesu Anafelanso M’bale Wako”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Khalani Munthu Wabwino Kwambili!.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 mapa. 1-11

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 82 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani