LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsa. 7
  • October 29–November 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 29–November 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 October tsa. 7

October 29–November 4

Yohane 18-19

  • Nyimbo 54 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Anacitila Umboni Coonadi”: (10 min.)

    • Yoh. 18:36—Coonadi cimakamba za Ufumu wa Mesiya

    • Yoh. 18:37—Yesu anacitila umboni coonadi cokhudza colinga ca Mulungu (“kudzacitila umboni coonadi,” “coonadi” nwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 18:38a—Zioneka kuti Pilato anatsutsa zakuti kuli coonadi (“Coonadi n’ciani?” nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 19:30—Kodi mawu akuti Yesu ‘anapeleka mzimu wake’ atanthauza ciani? (“kupeleka mzimu wake” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 19:31—Kodi pali umboni wabwanji woonetsa kuti Yesu anafa pa Nisani 14, mu 33 C.E.? (“Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 18:1-14

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno onetsani mwininyumba webusaiti yathu ya jw.org.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na funso lokakambilana ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 14 mapa. 6-7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 46

  • “Akhristu Oona Amadziŵika na Cikondi—Kondwelani na Coonadi”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Muzikondana”—Kondwelani ndi Coonadi Osati ndi Zosalungama. Ngati nthawi ilola, kambilanani kabokosi kakuti “Citsanzo ca m’Baibo Cofunika Kucisinkha-sinkha.”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 41

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 32 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani