LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsa. 7
  • Yesu Anacitila Umboni Coonadi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yesu Anacitila Umboni Coonadi
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 October tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 18-19

Yesu Anacitila Umboni Coonadi

18:36-38a

Yesu anacitila umboni coonadi cokhudza colinga ca Mulungu

  • M’MAWU: Mokangalika iye anali kulalikila coonadi conena za Ufumu wa Mulungu

  • M’ZOCITA: Umoyo wake unaonetsa poyela kuti maulosi a Mulungu amakwanilitsika

Pokhala ophunzila a Yesu, na ise timacitila umboni coonadi

  • M’MAWU: Ngakhale ena atinyoze, mokangalika timalalikila uthenga wabwino wonena za kukhazikitsidwa kwa Ufumu wa Mulungu, umene Khristu ndiye Mfumu yake

  • M’ZOCITA: Timaonetsa kuti tikucilikiza ufumu wa Yesu mwa kuyesetsa kukhala na makhalidwe aumulungu komanso mwa kupewa kutengako mbali m’zandale

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu onidziŵa amaona kuti nimakonda kucitila umboni coonadi?’

Alongo akutambitsa mzimayi vidiyo; m’bale akulalikila munthu m’galaji; makolo na ana akucita kulambila kwa pabanja; mlongo akulalikila mnzake wa kunchito
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani