LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsa. 2
  • December 3-9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 3-9
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 December tsa. 2

December 3-9

MACHITIDWE 9-11

  • Nyimbo 115 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Wozunza Akhristu Mwankhaza Akhala Mlaliki Wokangalika”: (10 min.)

    • Mac. 9:1, 2—Saulo anazunza ophunzila a Yesu mwankhanza (bt peji 60 pala. 1-2)

    • Mac. 9:15, 16—Saulo anasankhidwa kuti acitile umboni za Yesu (w16.06 peji 4 pala. 4)

    • Mac. 9:20-22—Saulo anakhala mlaliki wokangalika (bt peji 64 pala. 15)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 9:4—N’cifukwa ciani Yesu anafunsa Saulo kuti: “N’cifukwa ciani ukundizunza?” (bt mape. 60-61 mapa. 5-6)

    • Mac. 10:6—N’cifukwa ciani n’zocititsa cidwi kuti mtumwi Petulo anakakhala kunyumba kwa wofufuta zikopa? (“Simoni wina wofufuta zikopa” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 9:10-22

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) jl phunzilo 6

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya December.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 44

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 59 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani