LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsa. 6
  • March 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 March tsa. 6

March 25-31

1 AKORINTO 4-6

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Cofufumitsa Cacing’ono Cimafufumitsa Mtanda Wonse”: (10 min.)

    • 1 Akor. 5:1, 2—Mpingo wa ku Korinto unali kulekelela munthu wocita zoipa wosalapa

    • 1 Akor. 5:5-8, 13—Paulo anauza mpingowo kuti ucotse “cofufumitsa” pakati pawo na kupeleka wocita zoipayo kwa Satana (it-2 230, 869-870)

    • 1 Akor. 5:9-11—Mpingo suyenela kuyanjana ndi anthu ocita zoipa amene safuna kulapa (lvs 241, mfundo za kumapeto “Kucotsa Munthu mu Mpingo”)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Akor. 4:9—Kodi atumiki a Mulungu aumunthu ni “coonetsedwa m’bwalo la maseŵela” kwa angelo motani? (w09 5/15 24 ¶16)

    • 1 Akor. 6:3—Kodi Paulo ayenela kuti anatanthauza ciani pamene analemba kuti: “Tidzaweluza angelo”? (it-2 211)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 6:1-14 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs peji 44 (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 78

  • “Seŵenzetsani Mavidiyo Pophunzitsa Anthu Baibo”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani na kukambilana vidiyo yoonetsa wofalitsa akuseŵenzetsa vidiyo ya phunzilo 4 m’bulosha ya Uthenga Wabwino, pophunzitsa wophunzila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 60

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 23 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani