LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsa. 6
  • April 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 April tsa. 6

April 22-28

1 AKORINTO 14-16

  • Nyimbo 22 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Adzakhala ‘Zinthu Zonse kwa Aliyense’” (10 min.)

    • 1 Akor. 15:24, 25—Ufumu wa Mesiya udzawononga adani onse a Mulungu (w98 7/1 21 ¶10)

    • 1 Akor. 15:26—Imfa idzawonongedwa (kr 237 ¶21)

    • 1 Akor. 15:27, 28—Khristu adzapeleka Ufumu kwa Yehova (w12 9/15 12 ¶17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Akor. 14:34, 35—Kodi mtumwi Paulo analetsa akazi kulankhula? (w12 9/1 9, bokosi)

    • 1 Akor. 15:53—Kodi mawu akuti kusafa na kusawonongeka atanthauza ciani? (it-1 1197-1198)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 14:20-40 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 69

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 63

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 103 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani