LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsa. 6
  • Mulungu Adzakhala “Zinthu Zonse kwa Aliyense”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mulungu Adzakhala “Zinthu Zonse kwa Aliyense”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Amakwanilitsa Malonjezo Ake Nthawi Zonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Mukhale Oyela”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • “Tsopano Uona Zimene Ndicite kwa Farao”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Kodi Mumasunga Malonjezo Anu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 April tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 AKORINTO 14-16

Mulungu Adzakhala “Zinthu Zonse kwa Aliyense”

15:24-28

Anthu okhulupilika kwa Yehova ayembekezela kudzakhala na tsogolo labwino. Tikamauzako ena mogwila mtima za ciyembekezo cathu, ciyembekezoco cimakhomelezeka mwa ife. Mtumwi Paulo analimbikitsa Akhristu anzake kuti aziganizila nthawi ya kumapeto kwa Ulamulilo wa Khristu wa Zaka 1000, pamene Yehova adzakhala “zinthu zonse kwa aliyense.”

Angelo ateteza anthu a Yehova pa cisautso cacikulu; anthu ali m’Paradaiso; Yesu avula cisoti cake cacifumu ndipo apeleka Ufumu kwa Yehova Mulungu

Ni madalitso ati amene muyembekezela mwacidwi kudzayaona? Nanga n’cifukwa ciani?

N’ciani cimakutsimikizilani kuti malonjezo a Mulungu adzakwanilitsidwa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani