LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsa. 7
  • April 29–May 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 29–May 5
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 April tsa. 7

April 29–May 5

2 AKORINTO 1-3

  • Nyimbo 44 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova ni ‘Mulungu Amene Amatitonthoza M’njila Iliyonse’”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Akorinto Waciŵili.]

    • 2 Akor. 1:3—Yehova ni “Tate wacifundo cacikulu” (w17.07 13 ¶4)

    • 2 Akor. 1:4—Timatonthoza ena cifukwa nafenso Yehova amatitonthoza (w17.07 15 ¶14)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 2 Akor. 1:22—Kodi “cikole” komanso “cidindo” cimene Mkhristu aliyense wodzozedwa amalandila kucokela kwa Mulungu ciani? (w16.04 32)

    • 2 Akor. 2:14-16—Kodi mtumwi Paulo ayenela kuti anatanthauza ciani pamene anakamba za ‘kuguba pa cionetselo conyadilila kupambana’? (w10 8/1 23)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Akor. 3:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 52-53 ¶3-4 (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 86

  • “Pitilizani Kulandila Maphunzilo Aumulungu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Olemela Mwauzimu Cifukwa Cophunzitsidwa na Yehova.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 64

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 130 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani