LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsa. 4
  • June 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 June tsa. 4

June 17-23

AEFESO 4-6

  • Nyimbo 71 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zocokela kwa Mulungu”: (10 min.)

    • Aef. 6:11-13—Tifunika kudziteteza kwa Satana na ziŵanda zake (w18.05 27 ¶1)

    • Aef. 6:14, 15—Dzitetezeni na coonadi, cilungamo, komanso uthenga wabwino wamtendele (w18.05 28-29 ¶4, 7, 10)

    • Aef. 6:16, 17—Dzitetezeni na cikhulupililo, ciyembekezo ca cipulumutso, komanso Mawu a Mulungu (w18.05 29-31 ¶13, 16, 20)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aef. 4:30—Kodi munthu angamvetse cisoni mzimu woyela wa Mulungu motani? (it-1 1128 ¶3)

    • Aef. 5:5—Kodi munthu waumbombo amakhala wopembedza mafano m’lingalilo lanji? (it-1 1006 ¶2)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aef. 4:17-32 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno, chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 135

  • “Kodi Yehova Aiona Bwanji Nkhaniyi?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Pitilizani Kuzindikila Cifunilo ca Yehova (Lev. 19:18).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 71

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani