LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsa. 3
  • July 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 July tsa. 3

July 8-14

1 ATESALONIKA 1-5

  • Nyimbo 90 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitilizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Atesalonika.]

    • 1 Ates. 5:11-13—Tiziŵapatsa “ulemu waukulu” amene amatsogolela pakati pathu (w11 6/15 26 ¶12; 28 ¶19)

    • 1 Ates. 5:14—Lankhulani molimbikitsa kwa anthu a mtima wacisoni, komanso thandizani ofooka (w17.10 10 ¶13; w15 2/15 9 ¶16)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Ates. 4:3-6—Kodi munthu akacita dama, ‘amaphwanyila ufulu m’bale wake’ m’njila yanji? (it-1 863-864)

    • 1 Ates. 4:15-17—N’ndani amene adzatengedwa “m’mitambo kukakumana ndi Ambuye m’mlengalenga”? Nanga zimenezi zidzacitika bwanji? (w15 7/15 18-19 ¶14-15)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Ates. 3:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 4)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 81

  • Apainiya Amalimbikitsa: (9 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Apainiya Amathandiza Kwambili. Pambuyo pake, yankhani mafunso aya: Kodi apainiya amalimbikitsa bwanji ena mu mpingo? Nanga imwe, apainiya a mu mpingo mwanu amakulimbikitsani bwanji?

  • Zitsanzo Zabwino Zimene Zimatilimbikitsa: (6 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Tifunika ‘Kuthamanga Mopilila’—Tengelani Zitsanzo Zabwino. Ndiyeno, yankhani mafunso otsatila: Kodi mlongoyu anali na vuto lanji? Nanga anacita ciani kuti athandizike?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 74

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 100 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani