LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsa. 7
  • August 26–September 1

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 26–September 1
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 August tsa. 7

August 26–September 1

AHEBERI 4-6

  • Nyimbo 5 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu”: (10 min.)

    • Aheb. 4:1, 4—Lidziŵeni tsiku la mpumulo wa Mulungu (w11 7/15 24-25 ¶3-5)

    • Aheb. 4:6—Muzimvela Yehova (w11 7/15 25 ¶6)

    • Aheb. 4:9-11—Pewani kukhala na mzimu wodzidalila (w11 7/15 28 ¶16-17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aheb. 4:12—Kodi “mawu a Mulungu” ochulidwa pa lembali n’ciani? (w16.09 13)

    • Aheb. 6:17, 18—Kodi “zinthu ziŵili zosasinthika” zochulidwa m’mavesiwa n’ciani? (it-1 1139 ¶2)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aheb. 5:1-14 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs 228-229 ¶7-8 (th phunzilo 12)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 75

  • “Nchito Zabwino Zimene Sizidzaiŵalidwa”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Dzipelekeni Kukacita Utumiki wa pa Beteli.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 81

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 12 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani