LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsa. 6
  • Amuna Anayi Okwela pa Mahosi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Amuna Anayi Okwela pa Mahosi
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Mau Oyamba
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Mmene Amuna Anayi Okwela pa Mahosi Amakukhudzilani
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Kodi Amuna Anayi Okwela pa Mahosi N’ndani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 November tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 4-6

Amuna Anayi Okwela pa Mahosi

6:2, 4-6, 8

Yesu wakwela pa hosi yoyela ndipo ali ndi uta m’dzanja lake; ndipo okwela pa hosi yofiila ngati moto, yakuda, komanso yotuŵa akumutsatila

Yesu ‘anapita kukagonjetsa adani ake’ mwa kumenya nkhondo na Satana ndi ziŵanda zake kumwamba na kuziponya pa dziko lapansi. Yesu akupitiliza kugonjetsa adani ake mwa kuthandiza na kuteteza atumiki ake m’masiku otsiliza ano. Pa Aramagedo, iye ‘adzapambana pa nkhondo yolimbana nawo’ pamene adzacotsapo amuna atatu okwela pa mahosi, komanso pamene adzakonza zinthu zimene iwo awononga.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani