LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsa. 7
  • Yehova Amakonda Munthu Wopeleka Mokondwela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amakonda Munthu Wopeleka Mokondwela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Mphamvu ya ‘Tumakobili Tuŵili Twatung’ono’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Okonzeka Kupeleka Mphatso kwa Yehova”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Ni Mphatso Yanji Imene Tingam’patse Yehova?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Muziyamikila Kuolowa Manja kwa Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 November tsa. 7
Mlongo ali na foni m’manja

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Yehova Amakonda Munthu Wopeleka Mokondwela

Pa 2 Akorinto 9:7, pamati: “Aliyense acite mogwilizana ndi mmene watsimikizila mumtima mwake, osati monyinyilika kapena mokakamizika, cifukwa Mulungu amakonda munthu wopeleka mokondwela.” Masiku ano, pali njila zosavuta zocitila copeleka pa intaneti kuti ticilikize nchito ya Mboni za Yehova, m’dziko lathu komanso padziko lonse.

TAMBITSANI VIDIYO YAKUTI MMENE MUNGAPELEKELE ZOPELEKA PA INTANETI, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AYA:

  • Pa foni komanso pa tabuleti paonetsa webusaiti ya jw.org

    Kodi peji yofotokoza njila za mocitila copeleka m’dziko lathu tingaipeze bwanji?

  • Banja likukambilana za copeleka ca mphatso zina

    Kodi ena apindula bwanji cifukwa cocita copeleka kupitila pa intaneti?

  • Zizindikilo za mocitila copeleka

    Ni njila zina ziti zimene tingaseŵenzetse pocita copeleka?

  • M’bale wacinyamata akuthandiza m’bale wacikulile mocitila copeleka pa intaneti

    Tingacite ciani ngati sitidziŵa kuseŵenzetsa njila za pa intaneti zimenezi?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani