July 20-26
EKSODO 10-11
Nyimbo 65 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mose na Aroni Anaonetsa Kulimba Mtima Kwambili”: (10 min.)
Eks 10:3-6—Molimba mtima Mose na Aroni analengeza mlili wa namba 8 kwa Farao (w09 7/15 20 ¶6)
Eks. 10:24-26—Mose na Aroni sanagonje pamene Farao anayesa kuwanyengelela kuti asalabadile zonse zimene Yehova anawalamula
Eks. 10:28; 11:4-8—Mopanda mantha Mose na Aroni analengeza mlili wa namba 10 (it-2 436 ¶4)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 10:1, 2—Kodi makolo angaphunzile ciani pa mavesiwa? (w95 9/1 11 ¶11)
Eks. 11:7—Kodi Yehova anatanthauza ciani pamene anakamba kuti “galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli”? (it-1 783 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks 10:1-15 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani mafunso otsatilawa: Kodi mwaphunzilapo ciani poona mmene wofalitsa wakambila na mwininyumba? Kodi wofalitsa akanacita ciani kuti agaŵile cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu?
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno Itanilani mwininyumba ku misonkhano. (th phunzilo 8)
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu. (th phunzilo 12)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kodi Zolengedwa Zimatiphunzitsa Ciani za Kulimba Mtima?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Tiphunzile Kulimba Mtima ku Zolengedwa.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 124
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 113 na Pemphelo