LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 September tsa. 5
  • September 21-27

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 21-27
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 September tsa. 5

September 21-27

EKSODO 27-28

  • Nyimbo 25 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kodi Tingaphunzile Ciani pa Zovala za Ansembe?”: (10 min.)

    • Eks. 28:30—Tifunika kufuna-funa citsogozo ca Yehova (it-2 1143)

    • Eks. 28:36—Tifunika kukhalabe oyela (it-1 849 ¶3)

    • Eks. 28:42, 43—Tifunika kucita zinthu mwaulemu polambila Yehova (w08 8/15 15 ¶17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Eks. 28:15-21—Kodi miyala yamtengo wapatali imene inali kuikidwa pacovala pacifuwa ca mkulu wa ansembe ku Isiraeli anali kuitenga kuti? (w12 8/1 26 ¶1-3)

    • Eks. 28:38—Kodi “zinthu zopatulika” zinali ciani? (it-1 1130 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 27:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kakhadi kongela pa jw.org. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu. (th phunzilo 2)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs 111 ¶20-21 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 57

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Anthu Amene Sanatuluke m’Nyumba”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani na kukambilana vidiyo yoyamba, ndiyeno tambitsani na kukambilana vidiyo yaciŵili.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) jy mutu 133

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 46 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani