LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 2
  • November 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 2

November 2-8

EKSODO 39-40

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mose Anatsatila Malangizo Mosamala”: (10 min.)

    • Eks. 39:32—Mose anatsatila mosamala malangizo a Yehova pomanga cihema (w11 9/15 27 ¶13)

    • Eks. 39:43—Mose anayendela cihema pamene cinatha kumangidwa

    • Eks. 40:1, 2, 16—Mose anautsa cihema mogwilizana na malangizo a Yehova (w05 7/15 27 ¶3)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Eks. 39:34—Kodi mwina n’cifukwa ciani Aisiraeli anakwanitsa kupeza zikopa za akatumbu zomangila cihema? (it-2 884 ¶3)

    • Eks. 40:34—Kodi mtambo umene unayamba kuphimba cihema cokumanako unacitila umboni ciani? (w15 7/15 21 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 39:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pa sikilini. Kambilanani mmene tingapewele kutengako mbali m’zandale ngati mwininyumba wayambitsa nkhani yandale kapena yokhudza mavuto a m’dziko.

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Yankhani funso la mwininyumba lofuna kudziŵa maganizo anu ponena za munthu winawake amene acita nawo mpikisano pandale kapena ponena za nkhani inayake yandale. (th phunzilo 12)

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w16.04 23-24 ¶8-10—Mutu: Kodi Tingapewe Bwanji Kutengako Mbali m’Ndale mwa Zokamba na Zoganiza Zathu? (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 123

  • Mvetsani Tanthauzo Lake (Mat. 13:16): (15 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Ndiyeno, funsani omvetsela mafunso aya: N’cifukwa ciani tiyenela kumvetsa tanthauzo lake? Kodi lemba la Maliko 4:23, 24 limatanthauza ciani? Kodi tingapeleke citsanzo cotani cothandiza kumvetsetsa tanthauzo la Aheberi 2:1? Kodi tingaonetse bwanji kuti tikumvetsa tanthauzo lake?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) jy mutu 139

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 139 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani