LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 2
  • Mose Anatsatila Malangizo Mosamala

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mose Anatsatila Malangizo Mosamala
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Kumvela Kumaposa Nsembe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Maguwa Ansembe a pa Cihema Komanso Nchito Yawo pa Kulambila Koona
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 39-40

Mose Anatsatila Malangizo Mosamala

39:32, 43; 40:1, 2, 16

Mose anatsatila mosamala malangizo a tsatane-tsatane amene Yehova anam’patsa a mmene anafunika kumangila cihema na kuciutsa. Nafenso tiyenela kumvela malangizo alionse amene timalandila m’gulu la Yehova, na kuwatsatila mwamsanga komanso na mtima wonse. Kucita zimenezi n’kofunika olo malangizo aoneke monga osafunika kapena ngati sitimvetsetsa cifukwa cimene atipatsila malangizowo.—Luka 16:10.

N’cifukwa ciani tiyenela kumvetsela na kutsatila mosamala malangizo amene timalandila . . .

  • pa kukumana kokonzekela ulaliki?

  • okhudza kukonzekela matenda a mwadzidzidzi?

  • okhudza kukonzekela matsoka a zacilengedwe?

Zithunzi: Abale na alongo akutsatila malangizo amene alandila. 1. Kagulu kasonkhana pakhonde kuti katenge malangizo a ulaliki. 2. Mlongo akulemba zosankha zake pa nkhani ya cithandizo ca mankhwala. Iye akulemba zosankhazo pa khadi ya DPA. 3. Banja likonzekela masoka a zacilengedwe mwa kuika zinthu zofunikila m’kacola.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani