April 18-24
1 SAMUELI 23–24
Nyimbo 114 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yembekezelani Yehova Moleza Mtima”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 23:16, 17—Tingatengele bwanji citsanzo ca Yonatani? (w17.11 27 ¶11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 23:24–24:7 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi Yathu (th phunzilo 13)
Nkhani: (Mph. 5) w19.03 23-24 ¶12-15 —Mutu: Muzileza Mtima na Anthu Amene Mumawaphunzitsa Baibo. (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Mayeso Onse Ali na Mapeto Ake”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Anthu Ogwilizana m’Dziko Logaŵikana.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 85
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 17 na Pemphelo