LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 10
  • Ndandanda ya 2022 ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya 2022 ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Ciŵelu, April 9
  • Sondo, April 10
  • Mande, April 11
  • Ciŵili, April 12
  • Citatu, April 13
  • Cinayi, April 14
  • Cisanu, April 15
  • Cikumbutso (Dzuŵa Litaloŵa)
  • Ciŵelu, April 16
  • Sondo, April 17
  • Mande, April 18
  • Ndandanda ya Kuwelenga Baibulo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2025
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2025
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2023
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo Ya Cikumbutso ca 2024
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
  • Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 10

Ndandanda ya 2022 ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso

Ciŵelu, April 9

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 8 iyamba)

  • Yohane 11:55–12:1

Sondo, April 10

Mariya akuthila mafuta onunkhila m’mutu mwa Yesu pamene iye akudya patebulo.

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 9 iyamba)

  • Mateyu 26:6-13

  • Maliko 14:3-9

  • Yohane 12:2-11

Yesu ndi Njira, mutu 101

Mande, April 11

Yesu wakwela bulu. Gulu la anthu likuyala zovala zawo na masamba a kanjedza mumsewu.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 21:1-11, 14-17

  • Maliko 11:1-11

  • Luka 19:29-44

  • Yohane 12:12-19

Yesu ndi Njira, mutu 102

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 10 iyamba)

Ciŵili, April 12

Yesu akugubuduza matebulo a osintha ndalama m’kacisi.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 21:12, 13, 18, 19

  • Maliko 11:12-19

  • Luka 19:45-48

  • Yohane 12:20-50

Yesu ndi Njira, mutu 103-104

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 11 iyamba)

Citatu, April 13

Yesu na ophunzila ake akuona mkazi wamasiye wosauka pamene akuponya tumakobili tuŵili twatung’ono moponyamo zopeleka m’kacisi.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 21:19–25:46

  • Maliko 11:20–13:37

  • Luka 20:1–21:38

Yesu ndi Njira, mutu 105-114

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 12 iyamba)

Cinayi, April 14

Yudasi Isikariyoti akupangila Yesu ciwembu pamodzi na atsogoleli acipembedzo.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 26:1-5, 14-16

  • Maliko 14:1, 2, 10, 11

  • Luka 22:1-6

Yesu ndi Njira, mutu 115

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 13 iyamba)

Cisanu, April 15

Cikumbutso (Dzuŵa Litaloŵa)

Yesu na ophunzila ake okhulupilika ali pa tebulo la cakudya pa nthawi ya M’gonelo wa Ambuye.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 26:17-19

  • Maliko 14:12-16

  • Luka 22:7-13

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 14 iyamba)

  • Mateyu 26:20-75

  • Maliko 14:17-72

  • Luka 22:14-65

  • Yohane 13:1–18:27

Yesu ndi Njira, mutu 116-126

Ciŵelu, April 16

Yesu ali pa mtengo wozunzikilapo, ndipo pambali pake papacikidwa wacifwamba.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 27:1-61

  • Maliko 15:1-47

  • Luka 22:66–23:56

  • Yohane 18:28–19:42

Yesu ndi Njira, mutu 127-133

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 15 iyamba)

Sondo, April 17

Atsogoleli acipembedzo akupempha zinazake kwa Pilato.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 27:62-66

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 16 iyamba)

  • Maliko 16:1

Mande, April 18

Akazi adabwa poona kuti m’manda a Yesu mulibe kanthu.

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Mateyu 28:1-15

  • Maliko 16:2-8

  • Luka 24:1-49

  • Yohane 20:1-25

Yesu ndi Njira, mutu 134-135

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 17 iyamba)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani