LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 15
  • “Cikondi . . . Sicidzikuza”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Cikondi . . . Sicidzikuza”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • “Cikondi . . . Cimayembekezela Zinthu Zonse”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 15
Zithunzi: 1. M’bale akupemphela asanayambe kuŵelenga Baibo. 2. Akuyeletsa m’Nyumba ya Ufumu. 3. Iye na mkazi wake apita kukaona mlongo wacikulile ku cipatala.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Cikondi . . . Sicidzikuza”

Cikondi cimatithandiza kukhala odzicepetsa. (1 Akor. 13:4) Ngati timakonda abale athu, sitidzadziona kuti ndife ofunika kwambili kuposa ena. Timaona zabwino mwa ena na kuseŵenzetsa maluso athu powathandiza. (Afil. 2:3, 4) Tikamaonetsa kwambili cikondi cotelo, m’pamenenso Yehova angatiseŵenzetse kwambili pocita cifunilo ca Yehova.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI KUMBUKILANI MMENE CIKONDI CILILI—SICIDZIKUZA, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi Abisalomu anali na mphatso zotani?

  • Kodi mphatsozo anaziseŵenzetsa bwanji molakwika?

  • Tingacite ciyani kuti tipewe kudzikuza?—Agal. 5:26

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani