LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 10
  • April 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Tumitu
  • UMOYO WATHU WACIKHRISTU
  • Nyimbo 98
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 10

April 10-16

2 MBIRI 8-9

  • Nyimbo 88 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 9:19—Kodi zifanizilo 12 za mikango zimene zinali patsogolo pa mpando wacifumu wa Solomo ziyenela kuti zinali kuimila ciyani? (it-2 1097)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 8:1-16 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu—Mat. 16:16. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 2)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 09 mfundo 6 (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 98

  • “Kufuna-funa Nzelu mwa Kuŵelenga Baibo Tsiku Lililonse”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 42 na mfundo ya kumapeto 4

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 131 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani