LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 8
  • May 29–June 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 29–June 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 8

May 29–June 4

2 MBIRI 28–29

  • Nyimbo 54 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mungamutumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 29:25—Kodi citsanzo ca Natani citiphunzitsa ciyani za madalitso amene timapeza tikalola Yehova kutiwongolela? (w12 2/15 24-25)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 28:1-11 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 19)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 6) lff phunzilo 10 mfundo 4 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 56

  • Yehova ni “Tate wa Ana Amasiye”: (Mph. 8) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 7)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 47

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani